Ezekieli 13:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 kutanthauza aneneri a mu Isiraeli amene akulosera zokhudza Yerusalemu, amene akuona masomphenya onena za mzindawo kuti mudzakhala mtendere+ pamene simudzakhala mtendere,”’ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.+ Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:16 Nsanja ya Olonda,5/1/1997, ptsa. 8-9
16 kutanthauza aneneri a mu Isiraeli amene akulosera zokhudza Yerusalemu, amene akuona masomphenya onena za mzindawo kuti mudzakhala mtendere+ pamene simudzakhala mtendere,”’ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.+