2 Mafumu 25:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Anthu ena onse amene anatsala mumzindamo, ndi anthu amene anapita kumbali ya mfumu ya Babulo, ndiponso anthu ena onse,+ Nebuzaradani mkulu wa asilikali olondera mfumu anawatenga kupita nawo ku ukapolo.+ Yeremiya 52:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ziwerengero za anthu amene Nebukadirezara anawatenga kupita nawo ku ukapolo ndi izi: m’chaka cha 7 cha ulamuliro wake, anatenga Ayuda 3,023.+
11 Anthu ena onse amene anatsala mumzindamo, ndi anthu amene anapita kumbali ya mfumu ya Babulo, ndiponso anthu ena onse,+ Nebuzaradani mkulu wa asilikali olondera mfumu anawatenga kupita nawo ku ukapolo.+
28 Ziwerengero za anthu amene Nebukadirezara anawatenga kupita nawo ku ukapolo ndi izi: m’chaka cha 7 cha ulamuliro wake, anatenga Ayuda 3,023.+