Maliro 3:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ndi bwino kuti munthu ayembekezere+ chipulumutso cha Yehova+ moleza mtima.+ Mateyu 10:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Musachite mantha+ ndi amene amapha thupi koma sangaphe moyo, m’malomwake, muziopa iye+ amene angathe kuwononga zonse ziwiri, moyo ndi thupi lomwe m’Gehena.*+
28 Musachite mantha+ ndi amene amapha thupi koma sangaphe moyo, m’malomwake, muziopa iye+ amene angathe kuwononga zonse ziwiri, moyo ndi thupi lomwe m’Gehena.*+