Yesaya 59:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iwo amangonyalanyaza njira yamtendere,+ ndipo m’njira zawo mulibe chilungamo.+ Misewu yawo aikhotetsakhotetsa.+ Palibe munthu aliyense woyenda mmenemo amene adzadziwe mtendere.+
8 Iwo amangonyalanyaza njira yamtendere,+ ndipo m’njira zawo mulibe chilungamo.+ Misewu yawo aikhotetsakhotetsa.+ Palibe munthu aliyense woyenda mmenemo amene adzadziwe mtendere.+