Salimo 22:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Anthu onse okhala kumalekezero a dziko lapansi adzakumbukira Yehova ndi kubwerera kwa iye.+Ndipo mafuko onse a anthu a mitundu ina adzagwada pamaso panu.+ Salimo 102:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mitundu ya anthu idzaopa dzina lanu, inu Yehova,+Ndipo mafumu onse a padziko lapansi adzaopa ulemerero wanu.+
27 Anthu onse okhala kumalekezero a dziko lapansi adzakumbukira Yehova ndi kubwerera kwa iye.+Ndipo mafuko onse a anthu a mitundu ina adzagwada pamaso panu.+
15 Mitundu ya anthu idzaopa dzina lanu, inu Yehova,+Ndipo mafumu onse a padziko lapansi adzaopa ulemerero wanu.+