Yesaya 26:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 M’tsiku limenelo,+ m’dziko la Yuda+ mudzaimbidwa nyimbo+ yakuti: “Ife tili ndi mzinda wolimba.+ Iye waika chipulumutso ngati mipanda ndiponso ngati chiunda chomenyerapo nkhondo.*+ 1 Akorinto 3:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ngati munthu aliyense wawononga kachisi wa Mulungu, Mulungu adzawononganso munthu ameneyo,+ pakuti kachisi wa Mulungu ndi woyera,+ ndipo kachisiyo+ ndinuyo.+ Chivumbulutso 19:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Zimenezi zitatha, ndinamva mawu ofuula kumwamba+ ngati mawu a khamu lalikulu, akuti: “Tamandani Ya,* anthu inu!+ Chipulumutso,+ ulemerero, ndi mphamvu ndi za Mulungu wathu,+
26 M’tsiku limenelo,+ m’dziko la Yuda+ mudzaimbidwa nyimbo+ yakuti: “Ife tili ndi mzinda wolimba.+ Iye waika chipulumutso ngati mipanda ndiponso ngati chiunda chomenyerapo nkhondo.*+
17 Ngati munthu aliyense wawononga kachisi wa Mulungu, Mulungu adzawononganso munthu ameneyo,+ pakuti kachisi wa Mulungu ndi woyera,+ ndipo kachisiyo+ ndinuyo.+
19 Zimenezi zitatha, ndinamva mawu ofuula kumwamba+ ngati mawu a khamu lalikulu, akuti: “Tamandani Ya,* anthu inu!+ Chipulumutso,+ ulemerero, ndi mphamvu ndi za Mulungu wathu,+