Salimo 105:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Funafunani Yehova ndiponso mphamvu zake.+Funafunani nkhope yake nthawi zonse.+ Yesaya 55:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Anthu inu funafunani Yehova pamene iye akupezekabe.+ Muitaneni akadali pafupi.+