Yesaya 29:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iweyo udzatsika moti uzidzalankhula uli pansi penipeni. Mawu ako azidzamveka otsika ngati akuchokera m’fumbi.+ Mawuwo adzachokera m’dothi ngati a wolankhula ndi mizimu, ndipo adzamveka ngati kulira kwa mbalame kuchokera m’fumbi.+
4 Iweyo udzatsika moti uzidzalankhula uli pansi penipeni. Mawu ako azidzamveka otsika ngati akuchokera m’fumbi.+ Mawuwo adzachokera m’dothi ngati a wolankhula ndi mizimu, ndipo adzamveka ngati kulira kwa mbalame kuchokera m’fumbi.+