Yesaya 10:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Kuwala kwa Isiraeli+ kudzasanduka moto+ ndipo Woyera wake adzasanduka lawi la moto.+ Iye adzayaka n’kunyeketsa udzu wake* ndi zitsamba zake zaminga+ pa tsiku limodzi. Hoseya 10:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Inu anthu a ku Beteli, wina adzakuchitaninso zimenezi chifukwa ndinu anthu oipitsitsa.+ Ndithu, mfumu ya Isiraeli adzaikhalitsa chete m’bandakucha.”+
17 Kuwala kwa Isiraeli+ kudzasanduka moto+ ndipo Woyera wake adzasanduka lawi la moto.+ Iye adzayaka n’kunyeketsa udzu wake* ndi zitsamba zake zaminga+ pa tsiku limodzi.
15 Inu anthu a ku Beteli, wina adzakuchitaninso zimenezi chifukwa ndinu anthu oipitsitsa.+ Ndithu, mfumu ya Isiraeli adzaikhalitsa chete m’bandakucha.”+