Nahumu 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Amadzudzula nyanja+ ndi kuiphwetsa ndipo amaumitsa mitsinje yonse.+ Basana ndi Karimeli afota+ ndipo maluwa a mitengo ya ku Lebanoni nawonso afota.
4 Amadzudzula nyanja+ ndi kuiphwetsa ndipo amaumitsa mitsinje yonse.+ Basana ndi Karimeli afota+ ndipo maluwa a mitengo ya ku Lebanoni nawonso afota.