Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yoswa 3:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 madzi otsika kuchokera kumtunda anayamba kuima. Madziwo anakwera m’mwamba, ndipo anasefukira n’kupanga damu,+ limene linafika kutali kwambiri. Izi zinachitikira ku Adamu, mzinda woyandikana ndi mzinda wa Zeretani.+ Koma madzi omwe anali kutsikira kunyanja ya Araba, imene ndiyo Nyanja Yamchere,+ anaphwa. Choncho, madzi a mtsinjewo anaduka, ndipo anthuwo anawolokera kutsidya lina, pafupi ndi Yeriko.

  • Salimo 74:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Ndinu amene munang’amba nthaka ndi kupanga akasupe ndi makwawa.+

      Inu munaumitsa mitsinje imene inali kukhala ndi madzi nthawi zonse.+

  • Yesaya 19:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Madzi adzauma m’nyanja, ndipo mtsinje udzakhala wopanda madzi ndi wouma.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena