Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 14:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Onsewa anagwirizana+ ndi kutsetserekera limodzi kuchigwa cha Sidimu,+ ku Nyanja Yamchere.+

  • Numeri 34:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 “‘Chigawo chanu chakum’mwera chiyenera kuyambira kuchipululu cha Zini, kumalire a Edomu.+ Malire anu a kum’mwera ayenera kuchokera kumathero a Nyanja Yamchere,+ kum’mawa.

  • Deuteronomo 3:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Ndinawapatsa Araba, Yorodano ndi tsidya lake la kum’mawa, kuchokera ku Kinereti*+ mpaka kunyanja ya Araba. Imeneyi ndi Nyanja Yamchere+ imene ili m’munsi mwa Pisiga,+ kotulukira dzuwa.

  • Yoswa 12:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Anali kulamuliranso chigwa cha Araba+ mpaka kunyanja ya Kinereti+ kumbali ya kum’mawa kwa nyanjayi, n’kukafikanso kunyanja ya Araba, yomwe ndi Nyanja Yamchere.+ Anali kulamulira kumbali ya kum’mawa kwa nyanjayi, cha ku Beti-yesimoti,+ mpaka kum’mwera, kumunsi kwa Pisiga.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena