Ezekieli 30:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndidzaumitsa ngalande zotuluka mumtsinje wa Nailo+ ndi kugulitsa dzikolo kwa anthu oipa.+ Ndidzachititsa kuti dzikolo ndi zonse zimene zili mmenemo ziwonongedwe ndi anthu achilendo.+ Ine Yehova, ndanena zimenezi.’+ Zekariya 10:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndidzadutsa panyanja, nyanjayo nditaigwetsera tsoka.+ Ndidzamenya mafunde a nyanjayo+ ndipo madzi onse a mtsinje wa Nailo adzauma.+ Kunyada kwa Asuri kudzathetsedwa+ ndipo ndodo yachifumu+ ya Iguputo idzachoka.+
12 Ndidzaumitsa ngalande zotuluka mumtsinje wa Nailo+ ndi kugulitsa dzikolo kwa anthu oipa.+ Ndidzachititsa kuti dzikolo ndi zonse zimene zili mmenemo ziwonongedwe ndi anthu achilendo.+ Ine Yehova, ndanena zimenezi.’+
11 Ndidzadutsa panyanja, nyanjayo nditaigwetsera tsoka.+ Ndidzamenya mafunde a nyanjayo+ ndipo madzi onse a mtsinje wa Nailo adzauma.+ Kunyada kwa Asuri kudzathetsedwa+ ndipo ndodo yachifumu+ ya Iguputo idzachoka.+