Yesaya 14:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndidzathyola Msuri amene ali m’dziko langa+ ndipo ndidzamupondaponda pamapiri anga.+ Goli lake lidzachoka pa iwo ndipo katundu wake adzachoka pamapewa awo.”+ Mika 5:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ameneyu adzabweretsa mtendere.+ Msuri akadzalowa m’dziko lathu, akadzaponda nsanja zathu zokhalamo,+ ife tidzamutumizira abusa 7, inde atsogoleri 8 a anthu kuti akathane naye.
25 Ndidzathyola Msuri amene ali m’dziko langa+ ndipo ndidzamupondaponda pamapiri anga.+ Goli lake lidzachoka pa iwo ndipo katundu wake adzachoka pamapewa awo.”+
5 Ameneyu adzabweretsa mtendere.+ Msuri akadzalowa m’dziko lathu, akadzaponda nsanja zathu zokhalamo,+ ife tidzamutumizira abusa 7, inde atsogoleri 8 a anthu kuti akathane naye.