Salimo 72:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 M’masiku ake, wolungama adzaphuka,+Ndipo padzakhala mtendere wochuluka kwa nthawi yonse pamene mwezi udzakhalepo.+ Yesaya 9:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pakuti kwa ife kwabadwa mwana.+ Ife tapatsidwa mwana wamwamuna,+ ndipo paphewa pake padzakhala ulamuliro.+ Iye adzapatsidwa dzina lakuti Mlangizi Wodabwitsa,+ Mulungu Wamphamvu,+ Atate Wosatha,+ Kalonga Wamtendere.+ Luka 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Ulemerero kwa Mulungu kumwambamwamba,+ ndipo pansi pano mtendere+ pakati pa anthu amene iye amakondwera nawo.”+
7 M’masiku ake, wolungama adzaphuka,+Ndipo padzakhala mtendere wochuluka kwa nthawi yonse pamene mwezi udzakhalepo.+
6 Pakuti kwa ife kwabadwa mwana.+ Ife tapatsidwa mwana wamwamuna,+ ndipo paphewa pake padzakhala ulamuliro.+ Iye adzapatsidwa dzina lakuti Mlangizi Wodabwitsa,+ Mulungu Wamphamvu,+ Atate Wosatha,+ Kalonga Wamtendere.+
14 “Ulemerero kwa Mulungu kumwambamwamba,+ ndipo pansi pano mtendere+ pakati pa anthu amene iye amakondwera nawo.”+