Zekariya 10:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndidzadutsa panyanja, nyanjayo nditaigwetsera tsoka.Ndidzamenya mafunde a nyanjayo,+Ndipo madzi onse a mtsinje wa Nailo adzauma. Kunyada kwa Asuri kudzathetsedwa,Ndipo ndodo yachifumu ya Iguputo idzachoka.+
11 Ndidzadutsa panyanja, nyanjayo nditaigwetsera tsoka.Ndidzamenya mafunde a nyanjayo,+Ndipo madzi onse a mtsinje wa Nailo adzauma. Kunyada kwa Asuri kudzathetsedwa,Ndipo ndodo yachifumu ya Iguputo idzachoka.+