Zekariya 10:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndidzadutsa panyanja, nyanjayo nditaigwetsera tsoka.+ Ndidzamenya mafunde a nyanjayo+ ndipo madzi onse a mtsinje wa Nailo adzauma.+ Kunyada kwa Asuri kudzathetsedwa+ ndipo ndodo yachifumu+ ya Iguputo idzachoka.+
11 Ndidzadutsa panyanja, nyanjayo nditaigwetsera tsoka.+ Ndidzamenya mafunde a nyanjayo+ ndipo madzi onse a mtsinje wa Nailo adzauma.+ Kunyada kwa Asuri kudzathetsedwa+ ndipo ndodo yachifumu+ ya Iguputo idzachoka.+