Yesaya 19:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Uwu ndi uthenga wokhudza Iguputo:+ Taonani! Yehova wakwera mtambo wothamanga ndipo akubwera mu Iguputo. Milungu yopanda pake ya ku Iguputo idzanjenjemera pamaso pake,+Ndipo mitima ya anthu a ku Iguputo idzachita mantha kwambiri. Ezekieli 30:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: ‘Ndidzawononganso mafano onyansa* nʼkuthetsa milungu yopanda pake ya ku Nofi.*+ Sipadzapezekanso kalonga* wochokera mʼdziko la Iguputo ndipo ndidzachititsa kuti anthu amʼdzikolo azikhala mwamantha.+
19 Uwu ndi uthenga wokhudza Iguputo:+ Taonani! Yehova wakwera mtambo wothamanga ndipo akubwera mu Iguputo. Milungu yopanda pake ya ku Iguputo idzanjenjemera pamaso pake,+Ndipo mitima ya anthu a ku Iguputo idzachita mantha kwambiri.
13 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: ‘Ndidzawononganso mafano onyansa* nʼkuthetsa milungu yopanda pake ya ku Nofi.*+ Sipadzapezekanso kalonga* wochokera mʼdziko la Iguputo ndipo ndidzachititsa kuti anthu amʼdzikolo azikhala mwamantha.+