2 Mafumu 16:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Pomalizira pake, Ahazi anagona pamodzi ndi makolo ake ndipo anaikidwa m’manda mu Mzinda wa Davide+ pamodzi ndi makolo ake. Kenako Hezekiya+ mwana wake anayamba kulamulira m’malo mwake. 2 Mbiri 28:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Pomalizira pake, Ahazi anagona pamodzi ndi makolo ake ndipo anaikidwa m’manda mumzinda, ku Yerusalemu. Iye sanaikidwe m’manda a mafumu a Isiraeli.+ Kenako Hezekiya mwana wake anayamba kulamulira m’malo mwake.
20 Pomalizira pake, Ahazi anagona pamodzi ndi makolo ake ndipo anaikidwa m’manda mu Mzinda wa Davide+ pamodzi ndi makolo ake. Kenako Hezekiya+ mwana wake anayamba kulamulira m’malo mwake.
27 Pomalizira pake, Ahazi anagona pamodzi ndi makolo ake ndipo anaikidwa m’manda mumzinda, ku Yerusalemu. Iye sanaikidwe m’manda a mafumu a Isiraeli.+ Kenako Hezekiya mwana wake anayamba kulamulira m’malo mwake.