2 Mbiri 21:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Yehoramu anali ndi zaka 32 pamene anayamba kulamulira ndipo analamulira ku Yerusalemu zaka 8. Pomalizira pake iye anapita popanda womumvera chisoni.+ Choncho anamuika m’manda mu Mzinda wa Davide,+ koma osati m’manda a mafumu.+ 2 Mbiri 33:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Pomalizira pake Manase anagona pamodzi ndi makolo ake,+ ndipo anamuika m’manda+ panyumba yake. Kenako Amoni+ mwana wake anayamba kulamulira m’malo mwake. Miyambo 10:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Anthu akamakumbukira zabwino zimene munthu wolungama anali kuchita, amam’dalitsa,+ koma dzina la anthu oipa lidzawola.+
20 Yehoramu anali ndi zaka 32 pamene anayamba kulamulira ndipo analamulira ku Yerusalemu zaka 8. Pomalizira pake iye anapita popanda womumvera chisoni.+ Choncho anamuika m’manda mu Mzinda wa Davide,+ koma osati m’manda a mafumu.+
20 Pomalizira pake Manase anagona pamodzi ndi makolo ake,+ ndipo anamuika m’manda+ panyumba yake. Kenako Amoni+ mwana wake anayamba kulamulira m’malo mwake.
7 Anthu akamakumbukira zabwino zimene munthu wolungama anali kuchita, amam’dalitsa,+ koma dzina la anthu oipa lidzawola.+