Deuteronomo 11:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “Pakuti dziko limene mukupita kukalitenga kukhala lanu, si lofanana ndi dziko la Iguputo limene munatulukamo. Kumeneko munali kufesa mbewu zanu ndi kuzithirira ndi mapazi* anu, ngati kuti mukuthirira dimba la ndiwo zamasamba. Ezekieli 29:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Choncho, iwe ndikulanga ndi kuwononga ngalande zako zotuluka mu Nailo.+ Dziko la Iguputo ndiliwononga. Ndilisandutsa malo ouma komanso bwinja,+ kuchokera ku Migidoli+ mpaka ku Seyene+ kukafika kumalire a dziko la Itiyopiya.
10 “Pakuti dziko limene mukupita kukalitenga kukhala lanu, si lofanana ndi dziko la Iguputo limene munatulukamo. Kumeneko munali kufesa mbewu zanu ndi kuzithirira ndi mapazi* anu, ngati kuti mukuthirira dimba la ndiwo zamasamba.
10 Choncho, iwe ndikulanga ndi kuwononga ngalande zako zotuluka mu Nailo.+ Dziko la Iguputo ndiliwononga. Ndilisandutsa malo ouma komanso bwinja,+ kuchokera ku Migidoli+ mpaka ku Seyene+ kukafika kumalire a dziko la Itiyopiya.