-
2 Mafumu 10:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Chotero, amene anali kuyang’anira nyumba ya mfumu, ndi amene anali kuyang’anira mzinda, ndiponso akuluakulu komanso amene ankasamalira+ Ahabu, anatumiza uthenga kwa Yehu, wakuti: “Ife ndife atumiki anu, ndipo tichita chilichonse chimene mungatiuze. Sitisankha munthu aliyense kuti akhale mfumu yathu. Inuyo chitani chilichonse chimene mukuona kuti n’chabwino.”
-