2 Mafumu 10:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ku Samariya+ kunali ana aamuna a Ahabu okwanira 70.+ Chotero Yehu analemba makalata n’kuwatumiza kwa atsogoleri+ a ku Yezereeli, kwa akuluakulu,+ ndi kwa anthu amene ankasamalira ana a Ahabu ku Samariya. M’makalatamo analembamo kuti:
10 Ku Samariya+ kunali ana aamuna a Ahabu okwanira 70.+ Chotero Yehu analemba makalata n’kuwatumiza kwa atsogoleri+ a ku Yezereeli, kwa akuluakulu,+ ndi kwa anthu amene ankasamalira ana a Ahabu ku Samariya. M’makalatamo analembamo kuti: