Mateyu 18:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “Ndithu ndikukuuzani anthu inu, zilizonse zimene mudzamanga padziko lapansi zidzakhala zitamangidwa kumwamba, ndipo zilizonse zimene mudzamasula padziko lapansi zidzakhala zitamasulidwa kumwamba.+
18 “Ndithu ndikukuuzani anthu inu, zilizonse zimene mudzamanga padziko lapansi zidzakhala zitamangidwa kumwamba, ndipo zilizonse zimene mudzamasula padziko lapansi zidzakhala zitamasulidwa kumwamba.+