Salimo 46:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mitundu ya anthu inachita phokoso,+ maufumu anagwedezeka.Iye anatulutsa mawu ndipo dziko lapansi linasungunuka.+ Ezekieli 27:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Tsopano nyanja yakuwononga, ndipo wamira m’madzi ozama.+ Katundu wako wamalonda ndi khamu la anthu+ limene linali mwa iwe zatheratu.
6 Mitundu ya anthu inachita phokoso,+ maufumu anagwedezeka.Iye anatulutsa mawu ndipo dziko lapansi linasungunuka.+
34 Tsopano nyanja yakuwononga, ndipo wamira m’madzi ozama.+ Katundu wako wamalonda ndi khamu la anthu+ limene linali mwa iwe zatheratu.