Levitiko 10:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kutinso muziphunzitsa ana a Isiraeli+ malamulo onse amene Yehova wanena kwa iwo kudzera mwa Mose.” Malaki 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Wansembe ayenera kuphunzitsa anthu kuti adziwe Mulungu. Anthuwo ayenera kufunafuna kumva chilamulo kuchokera pakamwa pake,+ pakuti iye ndi mthenga wa Yehova wa makamu.+
11 Kutinso muziphunzitsa ana a Isiraeli+ malamulo onse amene Yehova wanena kwa iwo kudzera mwa Mose.”
7 Wansembe ayenera kuphunzitsa anthu kuti adziwe Mulungu. Anthuwo ayenera kufunafuna kumva chilamulo kuchokera pakamwa pake,+ pakuti iye ndi mthenga wa Yehova wa makamu.+