Miyambo 1:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Nzeru yeniyeni+ imangokhalira kufuula mumsewu.+ Imangokhalira kutulutsa mawu ake m’mabwalo a mzinda.+ Yeremiya 7:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Imirira pachipata cha nyumba ya Yehova, ndi kulengeza kuti,+ ‘Tamverani mawu a Yehova nonsenu okhala mu Yuda, amene mumalowa pazipata izi kuti mukagwadire Yehova.
20 Nzeru yeniyeni+ imangokhalira kufuula mumsewu.+ Imangokhalira kutulutsa mawu ake m’mabwalo a mzinda.+
2 “Imirira pachipata cha nyumba ya Yehova, ndi kulengeza kuti,+ ‘Tamverani mawu a Yehova nonsenu okhala mu Yuda, amene mumalowa pazipata izi kuti mukagwadire Yehova.