Yeremiya 6:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Monga mmene chitsime chimasungira madzi ake ali ozizira, Yerusalemu wasunga zoipa zake ngati zinthu zabwino. Mkati mwake mumamveka zachiwawa ndi kufunkha.+ Nthawi zonse ndimaona matenda ndi miliri mumzindawo.
7 Monga mmene chitsime chimasungira madzi ake ali ozizira, Yerusalemu wasunga zoipa zake ngati zinthu zabwino. Mkati mwake mumamveka zachiwawa ndi kufunkha.+ Nthawi zonse ndimaona matenda ndi miliri mumzindawo.