2 Mafumu 22:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 “N’chifukwa chake ndidzakugoneka+ pamodzi ndi makolo ako, ndipo ndithu udzaikidwa m’manda ako mu mtendere.+ Maso ako sadzaona tsoka lonse limene ndikulibweretsa pamalo ano.”’” Choncho iwo anabweretsa mawuwo kwa mfumuyo.
20 “N’chifukwa chake ndidzakugoneka+ pamodzi ndi makolo ako, ndipo ndithu udzaikidwa m’manda ako mu mtendere.+ Maso ako sadzaona tsoka lonse limene ndikulibweretsa pamalo ano.”’” Choncho iwo anabweretsa mawuwo kwa mfumuyo.