Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 7:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Tsopano chifukwa chakuti mwapitiriza kuchita ntchito zimenezi,’ watero Yehova, ‘ndipo ndinali kukulankhulani nthawi zonse, kudzuka m’mamawa ndi kukulankhulani,+ koma inu osamva,+ kukuitanani koma inu osandiyankha,+

  • Yeremiya 29:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Ndidzawachitira zimenezi chifukwa chakuti sanamvere mawu anga amene ndinali kuwatumizira kudzera mwa atumiki anga aneneri. Ndinali kudzuka m’mawa kwambiri ndi kutumiza atumiki angawo,’+ watero Yehova.

      “‘Inunso simunandimvere,’+ watero Yehova.

  • Yeremiya 44:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Ine ndinali kukutumizirani atumiki anga onse aneneri, kudzuka m’mawa kwambiri ndi kuwatumiza.+ Ndinali kuwatuma uthenga wakuti: “Chonde, musachite zinthu zonyansa zoterezi zimene ndimadana nazo.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena