Salimo 79:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 79 Inu Mulungu, anthu a mitundu ina alowa mādziko limene ndilo cholowa chanu.+Aipitsa kachisi wanu woyera.+Awononga Yerusalemu ndi kumusandutsa bwinja.+
79 Inu Mulungu, anthu a mitundu ina alowa mādziko limene ndilo cholowa chanu.+Aipitsa kachisi wanu woyera.+Awononga Yerusalemu ndi kumusandutsa bwinja.+