2 Mafumu 25:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Akasidiwo anatenganso ndowa, mafosholo, zozimitsira nyale, makapu, ndi ziwiya zonse+ zamkuwa zimene ansembe anali kugwiritsira ntchito potumikira. 2 Mbiri 36:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Mfumuyo inatenga ziwiya zonse,+ zazikulu+ ndi zazing’ono, za m’nyumba ya Mulungu woona. Inatenganso chuma+ cha m’nyumba ya Yehova, chuma cha mfumu+ ndi cha akalonga ake. Inatenga chilichonse n’kupita nacho ku Babulo.
14 Akasidiwo anatenganso ndowa, mafosholo, zozimitsira nyale, makapu, ndi ziwiya zonse+ zamkuwa zimene ansembe anali kugwiritsira ntchito potumikira.
18 Mfumuyo inatenga ziwiya zonse,+ zazikulu+ ndi zazing’ono, za m’nyumba ya Mulungu woona. Inatenganso chuma+ cha m’nyumba ya Yehova, chuma cha mfumu+ ndi cha akalonga ake. Inatenga chilichonse n’kupita nacho ku Babulo.