Salimo 10:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 N’chifukwa chiyani woipa amanyoza Mulungu?+Mumtima mwake amati: “Simudzandiimba mlandu.”+ Yeremiya 27:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Yehova wandiuza kuti, ‘Upange zomangira ndiponso magoli,+ ndipo uzivale m’khosi mwako.+