2 Mafumu 24:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mfumu ya Babulo inatengera ku Babulo amuna onse olimba mtima okwana 7,000, amisiri ndi anthu omanga makoma achitetezo okwana 1,000, ndi amuna onse amphamvu omenya nkhondo.+
16 Mfumu ya Babulo inatengera ku Babulo amuna onse olimba mtima okwana 7,000, amisiri ndi anthu omanga makoma achitetezo okwana 1,000, ndi amuna onse amphamvu omenya nkhondo.+