Ezara 6:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Muziwapatsa zimenezi kuti nthawi zonse+ azipereka nsembe zoziziritsa mtima+ kwa Mulungu wakumwamba, ndiponso kuti azipempherera moyo wa mfumu ndi ana ake.+ Ezara 7:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Zonse zimene Mulungu wakumwamba+ walamula+ zokhudza nyumba yake, zichitike modzipereka kwambiri+ kuti mkwiyo usayakire dziko la mfumu ndiponso usayakire ana ake.+ 1 Timoteyo 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Muchite zimenezi m’malo mwa mafumu+ ndi m’malo mwa anthu onse apamwamba,+ kuti tikhale ndi moyo wabata ndi wamtendere, ndiponso kuti tikhale odzipereka kwa Mulungu mokwanira komanso tikhale oganiza bwino.+
10 Muziwapatsa zimenezi kuti nthawi zonse+ azipereka nsembe zoziziritsa mtima+ kwa Mulungu wakumwamba, ndiponso kuti azipempherera moyo wa mfumu ndi ana ake.+
23 Zonse zimene Mulungu wakumwamba+ walamula+ zokhudza nyumba yake, zichitike modzipereka kwambiri+ kuti mkwiyo usayakire dziko la mfumu ndiponso usayakire ana ake.+
2 Muchite zimenezi m’malo mwa mafumu+ ndi m’malo mwa anthu onse apamwamba,+ kuti tikhale ndi moyo wabata ndi wamtendere, ndiponso kuti tikhale odzipereka kwa Mulungu mokwanira komanso tikhale oganiza bwino.+