Yeremiya 33:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Yehova wa makamu wanena kuti, ‘M’dziko lino lopanda pake, lopanda anthu ndi lopanda ziweto+ ndi mizinda yake yonse, mudzakhala malo odyetserako ziweto kumene abusa adzalola ziweto zawo kugona pansi.’+ Ezekieli 36:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndidzachulukitsa anthu mwa inu. Ndidzachulukitsa nyumba yonse ya Isiraeli.+ M’mizinda mudzakhala anthu+ ndipo malo owonongeka adzamangidwanso.+
12 “Yehova wa makamu wanena kuti, ‘M’dziko lino lopanda pake, lopanda anthu ndi lopanda ziweto+ ndi mizinda yake yonse, mudzakhala malo odyetserako ziweto kumene abusa adzalola ziweto zawo kugona pansi.’+
10 Ndidzachulukitsa anthu mwa inu. Ndidzachulukitsa nyumba yonse ya Isiraeli.+ M’mizinda mudzakhala anthu+ ndipo malo owonongeka adzamangidwanso.+