Yeremiya 32:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Anthu adzagula minda m’dziko lino,+ dziko limene anthu inu mudzanena kuti: “Dziko ili ndi bwinja,+ lopanda munthu wokhalamo kapena nyama yoweta. Linaperekedwa m’manja mwa Akasidi.”’+ Yeremiya 51:62 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 62 Ukanene kuti, ‘Inu Yehova! Inu mwanena zowononga malo ano ndi kuwafafaniza kuti pasapezekenso chilichonse chokhalamo.+ Musapezeke munthu kapena chiweto koma mzindawo ukhale bwinja mpaka kalekale.’
43 Anthu adzagula minda m’dziko lino,+ dziko limene anthu inu mudzanena kuti: “Dziko ili ndi bwinja,+ lopanda munthu wokhalamo kapena nyama yoweta. Linaperekedwa m’manja mwa Akasidi.”’+
62 Ukanene kuti, ‘Inu Yehova! Inu mwanena zowononga malo ano ndi kuwafafaniza kuti pasapezekenso chilichonse chokhalamo.+ Musapezeke munthu kapena chiweto koma mzindawo ukhale bwinja mpaka kalekale.’