Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 51:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Pakuti Yehova adzatonthoza Ziyoni.+ Iye adzatonthozadi malo ake onse owonongedwa.+ Adzachititsa chipululu chake kukhala ngati Edeni+ ndi dera lake lachipululu kukhala ngati munda wa Yehova.+ Mwa iye mudzakhala kusangalala ndi kukondwera, kuyamikira ndi kuimba nyimbo.+

  • Yesaya 58:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Chifukwa cha inu, anthu adzamanga malo amene anawonongedwa kalekale.+ Inu mudzamanganso maziko amene akhalapo ku mibadwomibadwo.+ Mudzatchedwa otseka mipata ya mpanda,+ ndiponso okonzanso misewu yomwe anthu amakhala m’mphepete mwake.

  • Yesaya 61:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Iwo adzamanganso malo amene akhala owonongeka kwa nthawi yaitali.+ Adzamanga malo amene anasakazidwa kalekale.+ Adzakonzanso mizinda yowonongedwa,+ malo amene akhala osakazidwa ku mibadwomibadwo.

  • Amosi 9:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Pamenepo ndidzasonkhanitsa ndi kubwezeretsa anthu anga Aisiraeli amene anagwidwa ndi kutengedwa kupita ku ukapolo.+ Iwo adzamanga mizinda imene ili yabwinja ndi kukhalamo.+ Adzalima minda ya mpesa ndi kumwa vinyo wochokera m’mindayo. Adzalimanso minda ya zipatso ndi kudya zipatso zochokera m’mindayo.’+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena