Salimo 148:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Amazichititsa kukhalapobe kwamuyaya, ngakhalenso mpaka kalekale.+Iye wazikhazikitsira lamulo, ndipo silidzatha.+ Yesaya 54:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pakuti mapiri akhoza kuchotsedwa, ndipo zitunda zikhoza kugwedezeka,+ koma kukoma mtima kwanga kosatha sikudzachotsedwa kwa iwe,+ ndipo pangano langa la mtendere silidzagwedezeka,”+ watero Yehova, amene akukuchitira chifundo.+ Yeremiya 33:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 “Yehova wanena kuti, ‘Ngati anthu inu mungathe kuphwanya pangano langa loti kukhale usana ndi pangano langa loti kukhale usiku, kuti usana ndi usiku zisafike pa nthawi yake,+
6 Amazichititsa kukhalapobe kwamuyaya, ngakhalenso mpaka kalekale.+Iye wazikhazikitsira lamulo, ndipo silidzatha.+
10 Pakuti mapiri akhoza kuchotsedwa, ndipo zitunda zikhoza kugwedezeka,+ koma kukoma mtima kwanga kosatha sikudzachotsedwa kwa iwe,+ ndipo pangano langa la mtendere silidzagwedezeka,”+ watero Yehova, amene akukuchitira chifundo.+
20 “Yehova wanena kuti, ‘Ngati anthu inu mungathe kuphwanya pangano langa loti kukhale usana ndi pangano langa loti kukhale usiku, kuti usana ndi usiku zisafike pa nthawi yake,+