Salimo 119:91 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 91 Chilengedwe chonse chakhalapobe kufikira lero chifukwa cha zigamulo zanu,+Pakuti chilengedwe chonse chimakutumikirani.+ Yeremiya 31:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 “‘Ngati malamulo amenewa angachotsedwe pamaso panga,+ ndiye kuti anthu amene ndi mbewu ya Isiraeli sadzakhala mtundu wokhala pamaso panga nthawi zonse,’+ watero Yehova.” Yeremiya 33:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 “Yehova wanena kuti, ‘Monga momwedi ndinakhazikitsira pangano langa loti kukhale usana ndi usiku,+ malamulo anga akumwamba ndi dziko lapansi,+
91 Chilengedwe chonse chakhalapobe kufikira lero chifukwa cha zigamulo zanu,+Pakuti chilengedwe chonse chimakutumikirani.+
36 “‘Ngati malamulo amenewa angachotsedwe pamaso panga,+ ndiye kuti anthu amene ndi mbewu ya Isiraeli sadzakhala mtundu wokhala pamaso panga nthawi zonse,’+ watero Yehova.”
25 “Yehova wanena kuti, ‘Monga momwedi ndinakhazikitsira pangano langa loti kukhale usana ndi usiku,+ malamulo anga akumwamba ndi dziko lapansi,+