Yeremiya 27:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 ‘“Ziwiya zimenezi zidzapita ku Babulo+ ndipo zidzakhala kumeneko kufikira ine nditazikumbukira,”+ watero Yehova. “Ndipo ndidzazibweretsa ndi kuzibwezeretsa pamalo ano.”’”+
22 ‘“Ziwiya zimenezi zidzapita ku Babulo+ ndipo zidzakhala kumeneko kufikira ine nditazikumbukira,”+ watero Yehova. “Ndipo ndidzazibweretsa ndi kuzibwezeretsa pamalo ano.”’”+