Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 25:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Zipilala+ zamkuwa zimene zinali m’nyumba ya Yehova, zotengera zokhala ndi mawilo+ ndi chosungiramo madzi chamkuwa+ zimene zinali m’nyumba ya Yehova, Akasidi anaziphwanyaphwanya n’kutenga mkuwa wake kupita nawo ku Babulo.+

  • 2 Mbiri 36:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Mfumuyo inatenga ziwiya zonse,+ zazikulu+ ndi zazing’ono, za m’nyumba ya Mulungu woona. Inatenganso chuma+ cha m’nyumba ya Yehova, chuma cha mfumu+ ndi cha akalonga ake. Inatenga chilichonse n’kupita nacho ku Babulo.

  • Yeremiya 52:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Akasidiwo anatenganso ndowa, mafosholo,+ zozimitsira nyale,+ mbale zolowa,+ makapu ndi ziwiya zonse zamkuwa zimene ansembe anali kugwiritsira ntchito potumikira.+

  • Danieli 5:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Pa nthawi imeneyo anabweretsa ziwiya zagolide zimene anazitenga m’kachisi, m’nyumba ya Mulungu ku Yerusalemu. Kenako mfumuyo, nduna zake, adzakazi ake ndi akazi ake ena apambali anayamba kumwera m’ziwiyazo.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena