1 Mafumu 7:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Anaumba zipilala ziwiri zamkuwa.+ Kutalika kwa chipilala chilichonse kunali mikono 18, ndipo pankafunika chingwe chotalika mikono 12 kuti ayeze kuzungulira chipilala chilichonse.+ 2 Mbiri 4:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Anapanga zipilala ziwiri,+ mitu ya zipilala yozungulira+ imene anaiika pamwamba pa zipilala ziwirizo, ndiponso maukonde awiri+ okutira mitu iwiri yozungulira imene inali pamwamba pa zipilalazo.
15 Anaumba zipilala ziwiri zamkuwa.+ Kutalika kwa chipilala chilichonse kunali mikono 18, ndipo pankafunika chingwe chotalika mikono 12 kuti ayeze kuzungulira chipilala chilichonse.+
12 Anapanga zipilala ziwiri,+ mitu ya zipilala yozungulira+ imene anaiika pamwamba pa zipilala ziwirizo, ndiponso maukonde awiri+ okutira mitu iwiri yozungulira imene inali pamwamba pa zipilalazo.