2 Mafumu 20:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 ‘“Masiku akubwera pamene zinthu zonse zimene zili m’nyumba mwako,+ ndi zonse zimene makolo ako akhala akusunga kufikira lero, anthu adzazitenga n’kupita nazo ku Babulo.+ Palibe chidzatsale,”+ watero Yehova.
17 ‘“Masiku akubwera pamene zinthu zonse zimene zili m’nyumba mwako,+ ndi zonse zimene makolo ako akhala akusunga kufikira lero, anthu adzazitenga n’kupita nazo ku Babulo.+ Palibe chidzatsale,”+ watero Yehova.