Yeremiya 32:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Koma inu Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, mwandiuza kuti, ‘Gula mundawu ndi ndalama+ pamaso pa mboni,’+ ngakhale kuti mzindawu uperekedwa m’manja mwa Akasidi.”+
25 Koma inu Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, mwandiuza kuti, ‘Gula mundawu ndi ndalama+ pamaso pa mboni,’+ ngakhale kuti mzindawu uperekedwa m’manja mwa Akasidi.”+