Yeremiya 37:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pakuti ngakhale anthu inu mutapha gulu lonse lankhondo la Akasidi amene akumenyana nanu+ ndipo pangotsala amuna ovulala kwambiri pakati pawo,+ aliyense wa amenewo adzadzuka muhema wake ndi kubwera kudzatentha mzinda uno.”’”
10 Pakuti ngakhale anthu inu mutapha gulu lonse lankhondo la Akasidi amene akumenyana nanu+ ndipo pangotsala amuna ovulala kwambiri pakati pawo,+ aliyense wa amenewo adzadzuka muhema wake ndi kubwera kudzatentha mzinda uno.”’”