-
Yeremiya 21:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 ‘Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena kuti: “Anthu inu, ine ndichititsa zida zimene zili m’manja mwanu kukutembenukirani. Zimenezi ndi zida zimene mukugwiritsa ntchito pomenyana ndi mfumu ya Babulo+ ndi Akasidi+ amene azungulira kunja kwa mpanda wanu. Ndipo ndisonkhanitsa zida zanuzo pakati pa mzinda uwu.+
-