Deuteronomo 18:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pakati panu pasapezeke munthu wotentha mwana wake pamoto,*+ wolosera,+ wochita zamatsenga,+ woombeza,*+ wanyanga,+ 1 Mafumu 11:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pa nkhani imeneyi, Mulungu anali atamulamula kuti asatsatire milungu ina,+ koma iye sanasunge zimene Yehova analamula.
10 Pakati panu pasapezeke munthu wotentha mwana wake pamoto,*+ wolosera,+ wochita zamatsenga,+ woombeza,*+ wanyanga,+
10 Pa nkhani imeneyi, Mulungu anali atamulamula kuti asatsatire milungu ina,+ koma iye sanasunge zimene Yehova analamula.