1 Mafumu 6:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Kunena za nyumba ukumangayi, ukayenda motsatira malamulo+ anga ndi kusunga zigamulo+ zanga zonse ndi kuzitsatira,+ inenso ndidzakwaniritsadi mawu anga okhudza iweyo amene ndinalankhula kwa bambo ako Davide.+ 2 Mbiri 7:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Koma inuyo mukadzabwerera+ n’kusiya kutsatira malamulo anga+ amene ndakupatsani, komanso mukadzapita kukatumikira milungu ina+ ndi kuigwadira,+
12 “Kunena za nyumba ukumangayi, ukayenda motsatira malamulo+ anga ndi kusunga zigamulo+ zanga zonse ndi kuzitsatira,+ inenso ndidzakwaniritsadi mawu anga okhudza iweyo amene ndinalankhula kwa bambo ako Davide.+
19 Koma inuyo mukadzabwerera+ n’kusiya kutsatira malamulo anga+ amene ndakupatsani, komanso mukadzapita kukatumikira milungu ina+ ndi kuigwadira,+