Yeremiya 23:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma adzalumbira kuti, ‘Pali Yehova Mulungu wamoyo amene anatulutsa a m’nyumba ya Isiraeli ndi kuwabweretsa kuno kuchokera m’dziko la kumpoto komanso kuchokera m’mayiko onse kumene ndinawabalalitsira’ ndipo adzakhala m’dziko lawo.”+ Amosi 9:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “‘Ine ndidzawabzala panthaka yawo ndipo sadzazulidwanso m’dziko limene ndawapatsa,’+ watero Yehova Mulungu wanu.”
8 Koma adzalumbira kuti, ‘Pali Yehova Mulungu wamoyo amene anatulutsa a m’nyumba ya Isiraeli ndi kuwabweretsa kuno kuchokera m’dziko la kumpoto komanso kuchokera m’mayiko onse kumene ndinawabalalitsira’ ndipo adzakhala m’dziko lawo.”+
15 “‘Ine ndidzawabzala panthaka yawo ndipo sadzazulidwanso m’dziko limene ndawapatsa,’+ watero Yehova Mulungu wanu.”